Ndalira Lyrics
Ndalira Song Lyrics
You Already Know
Mmene Ndinkabadwa Iwe Kunalibeko
So I Can Leave By Myself Without You
Tinakumana Okulakula
Komwe Ndachoka Sumakuziwa
Tsono Ulibe Chifukwa Choti Undidzulile
Sindingakupangitse Kuti Undikonde No No
Mtima Wako Ulikwina Tivomeledze
Unandiuza Uzandikonda
Mtima Wanga Uzawusunga
But Maybe Tomorrow
I Dont See You
So I Say No To The Toucher That You Give
Mtima Waine Mwiniwake Ndi Mulungu
So I Say No To The Sorry That You Say
Mabala Ayine Achilitsa Ndi Mulungu
Go Away, Go Away
Usandikumbutse Kale Ndalila
Go Away, Go Away
Usandikumbutse Kale Ndalila
Mmene Tinkasanzikana
Munalibe Misonzi Mmaso Mwako
Sizinakuwawa
I Know That Is What You Wanted
I Know You Dont Love Me
Red Flag Inalipo
Koma Ndekha Mumtima I Had Hope You Will Changed
Ndepapita Nthawi Pang`Ono Ndinamva Zoti Uli Ndiwina
Ndikakuwona Pa Foni Ukumawoneka Happy
Nde Mukamayambana Ukumabwela Nditima Messege
Umvekele You Miss Me
Do You Need To Live The Lies
So I Say No To The Toucher That You Give
Mtima Waine Mwiniwake Ndi Mulungu
So I Say No To The Sorry That You Say
Mabala Ayine Achilitsa Ndi Mulungu
Go Away, Go Away
Usandikumbutse Kale Ndalila
Go Away, Go Away
Usandikumbutse Kale Ndalila
So I Say No To The Toucher That You Give
Mtima Waine Mwiniwake Ndi Mulungu
So I Say No To The Sorry That You Say
Mabala Ayine Achilitsa Ndi Mulungu
Go Away, Go Away
Usandikumbutse Kale Ndalila
Go Away, Go Away
Usandikumbutse Kale Ndalila
Community Thoughts .
0 CommentsLeave a Reply
Your email address will not be published. Required fields are marked *
No comments yet
Be the first to share your thoughts about these lyrics!